-
Levitiko 13:59Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
59 Limeneli ndi lamulo lokhudza nthenda ya khate yopezeka pachovala chaubweya wa nkhosa kapena chansalu, mulitali kapena mulifupi, kapena pachinthu chilichonse chopangidwa ndi chikopa, kuti wansembe adziwe chinthu choyenera kugamula kuti nʼchoyera kapena nʼchodetsedwa.”
-