Levitiko 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno wansembe adzapereke nsembe yopsereza ndi nsembe yambewu+ paguwa lansembe. Akatero, wansembe adzamuphimbira machimo,+ ndipo munthuyo adzakhala woyera.+
20 Ndiyeno wansembe adzapereke nsembe yopsereza ndi nsembe yambewu+ paguwa lansembe. Akatero, wansembe adzamuphimbira machimo,+ ndipo munthuyo adzakhala woyera.+