-
Levitiko 14:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Akaona nthendayo nʼkupeza kuti ili mʼmakoma a nyumba, ndipo ikuoneka ngati mawanga obiriwira mopitira ku chikasu kapena ofiirira, komanso mawangawo akuoneka kuti alowa mkati mwa khoma,
-