-
Levitiko 15:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Aliyense wokhudza chilichonse chimene munthuyo wakhalapo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo. Ndipo munthu wonyamula zinthu zimenezi azichapa zovala zake nʼkusamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.
-