Levitiko 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno munthuyo akachira nthenda yake yakukhayo, pazipita masiku 7 kuti akhale woyera. Kenako azichapa zovala zake nʼkusamba madzi otunga kumtsinje, ndipo iye adzakhala woyera.+
13 Ndiyeno munthuyo akachira nthenda yake yakukhayo, pazipita masiku 7 kuti akhale woyera. Kenako azichapa zovala zake nʼkusamba madzi otunga kumtsinje, ndipo iye adzakhala woyera.+