Levitiko 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Wansembe azipereka mbalame imodzi monga nsembe yamachimo ndipo inayo monga nsembe yopsereza. Ndiyeno wansembe azimuphimbira machimo pamaso pa Yehova chifukwa cha kukhako.+
30 Wansembe azipereka mbalame imodzi monga nsembe yamachimo ndipo inayo monga nsembe yopsereza. Ndiyeno wansembe azimuphimbira machimo pamaso pa Yehova chifukwa cha kukhako.+