Levitiko 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Akatero Aroni azibweretsa ngʼombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo, ndipo aziphimba machimo ake+ ndi a banja lake.* Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:6 Nsanja ya Olonda,2/15/1998, tsa. 123/1/1987, tsa. 31
6 Akatero Aroni azibweretsa ngʼombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo, ndipo aziphimba machimo ake+ ndi a banja lake.*