Levitiko 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno azitenga ena mwa magazi a ngʼombe yamphongoyo+ nʼkuwadontheza ndi chala chake patsogolo pa chivundikiro, mbali ya kumʼmawa. Azidontheza magaziwo ndi chala chake maulendo 7 patsogolo pa chivundikirocho.+
14 Ndiyeno azitenga ena mwa magazi a ngʼombe yamphongoyo+ nʼkuwadontheza ndi chala chake patsogolo pa chivundikiro, mbali ya kumʼmawa. Azidontheza magaziwo ndi chala chake maulendo 7 patsogolo pa chivundikirocho.+