Levitiko 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Akatero azisamba thupi lonse+ mʼmalo oyera nʼkuvala zovala zake.+ Kenako azituluka nʼkukapereka nsembe yake yopsereza+ ndi nsembe yopsereza ya anthuwo+ ndipo aziphimba machimo ake ndi a anthuwo.+
24 Akatero azisamba thupi lonse+ mʼmalo oyera nʼkuvala zovala zake.+ Kenako azituluka nʼkukapereka nsembe yake yopsereza+ ndi nsembe yopsereza ya anthuwo+ ndipo aziphimba machimo ake ndi a anthuwo.+