Levitiko 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Limeneli ndi sabata lanu lopuma pa ntchito zonse ndipo muzisonyeza kuti mukudzimvera chisoni chifukwa cha machimo anu.+ Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:31 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Galamukani!,3/8/1995, tsa. 9
31 Limeneli ndi sabata lanu lopuma pa ntchito zonse ndipo muzisonyeza kuti mukudzimvera chisoni chifukwa cha machimo anu.+ Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale.