Levitiko 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwamuna aliyense pakati panu asayandikire wachibale wake aliyense kuti agone naye.*+ Ine ndine Yehova.
6 Mwamuna aliyense pakati panu asayandikire wachibale wake aliyense kuti agone naye.*+ Ine ndine Yehova.