Levitiko 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ukakwatira mkazi usakwatirenso mchemwali wake kuti akhale mkazi wako wachiwiri,+ nʼkumagona naye mchemwali wakeyo ali moyo.
18 Ukakwatira mkazi usakwatirenso mchemwali wake kuti akhale mkazi wako wachiwiri,+ nʼkumagona naye mchemwali wakeyo ali moyo.