Levitiko 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma inu muzisunga malamulo anga ndi zigamulo zanga.+ Ndipo aliyense wa inu, kaya ndi nzika kapena mlendo wokhala pakati panu, asamachite chilichonse cha zinthu zonyansa zimenezi.+
26 Koma inu muzisunga malamulo anga ndi zigamulo zanga.+ Ndipo aliyense wa inu, kaya ndi nzika kapena mlendo wokhala pakati panu, asamachite chilichonse cha zinthu zonyansa zimenezi.+