Levitiko 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mukamakolola zinthu zamʼmunda mwanu, musamachotseretu zonse mʼmphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha* mʼmunda mwanumo.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:9 Nsanja ya Olonda,6/15/2006, ptsa. 22-2312/1/2003, tsa. 17
9 Mukamakolola zinthu zamʼmunda mwanu, musamachotseretu zonse mʼmphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha* mʼmunda mwanumo.+