-
Levitiko 19:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Ndiyeno mʼchaka cha 5, mungathe kukolola zipatso zake mofanana ndi mbewu zina zonse komanso kudya zipatso za mtengowo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
-