Levitiko 19:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ngati munthu akukhala mʼdziko lanu monga mlendo, musamamuchitire zoipa.+