Levitiko 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu akakhala ndi chilema chilichonse, asayandikire malo opatulika. Kaya akhale ndi vuto losaona, wolumala, wankhope yopotoka,* wamkono kapena mwendo wautali kwambiri kuposa unzake,
18 Munthu akakhala ndi chilema chilichonse, asayandikire malo opatulika. Kaya akhale ndi vuto losaona, wolumala, wankhope yopotoka,* wamkono kapena mwendo wautali kwambiri kuposa unzake,