Levitiko 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma asamayandikire katani+ ndiponso guwa lansembe,+ chifukwa iye ali ndi chilema. Asadetse malo anga opatulika,+ chifukwa ine ndine Yehova amene ndikuwayeretsa.’”+
23 Koma asamayandikire katani+ ndiponso guwa lansembe,+ chifukwa iye ali ndi chilema. Asadetse malo anga opatulika,+ chifukwa ine ndine Yehova amene ndikuwayeretsa.’”+