Levitiko 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musamaphe ngʼombe kapena nkhosa ndi mwana wake pa tsiku limodzi.+