Levitiko 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuchokera pa tsiku lotsatana ndi Sabata, pamene munabweretsa mtolo kuti ukhale nsembe yoyendetsa uku ndi uku,+ muziwerenga masabata 7, ndipo sabata iliyonse izikhala ndi masiku okwanira.
15 Kuchokera pa tsiku lotsatana ndi Sabata, pamene munabweretsa mtolo kuti ukhale nsembe yoyendetsa uku ndi uku,+ muziwerenga masabata 7, ndipo sabata iliyonse izikhala ndi masiku okwanira.