-
Levitiko 23:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Munthu aliyense wogwira ntchito iliyonse pa tsiku limeneli, ndidzamuwononga nʼkumuchotsa pakati pa anthu a mtundu wake.
-