Levitiko 23:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pa tsiku la 15 la mwezi wa 7, mukakolola zinthu zamʼmunda mwanu, muzichita chikondwerero cha Yehova masiku 7.+ Tsiku loyamba la chikondwererocho ndi tsiku lopuma pa ntchito zanu zonse, ndipo muzipumanso pa ntchito zanu zonse pa tsiku la 8.+
39 Pa tsiku la 15 la mwezi wa 7, mukakolola zinthu zamʼmunda mwanu, muzichita chikondwerero cha Yehova masiku 7.+ Tsiku loyamba la chikondwererocho ndi tsiku lopuma pa ntchito zanu zonse, ndipo muzipumanso pa ntchito zanu zonse pa tsiku la 8.+