Levitiko 23:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 kuti mibadwo yanu ya mʼtsogolo idzadziwe+ kuti ine ndinachititsa Aisiraeli kukhala mʼmisasa powatulutsa mʼdziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”
43 kuti mibadwo yanu ya mʼtsogolo idzadziwe+ kuti ine ndinachititsa Aisiraeli kukhala mʼmisasa powatulutsa mʼdziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”