Levitiko 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pagulu lililonse la mikateyo uike lubani weniweni. Lubaniyo aziperekedwa nsembe yowotcha pamoto+ kwa Yehova kuimira nsembe yonseyo.
7 Pagulu lililonse la mikateyo uike lubani weniweni. Lubaniyo aziperekedwa nsembe yowotcha pamoto+ kwa Yehova kuimira nsembe yonseyo.