Levitiko 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu amene wamenya nʼkupha chiweto cha mnzake azilipira,+ koma amene wamenya nʼkupha munthu nayenso aziphedwa.+
21 Munthu amene wamenya nʼkupha chiweto cha mnzake azilipira,+ koma amene wamenya nʼkupha munthu nayenso aziphedwa.+