Levitiko 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno mʼmwezi wa 7, pa tsiku la 10 la mweziwo, muzidzaliza lipenga la nyanga ya nkhosa mokweza kwambiri. Pa Tsiku Lochita Mwambo Wophimba Machimo,+ muzidzaliza lipengalo kuti limveke mʼdziko lanu lonse.
9 Ndiyeno mʼmwezi wa 7, pa tsiku la 10 la mweziwo, muzidzaliza lipenga la nyanga ya nkhosa mokweza kwambiri. Pa Tsiku Lochita Mwambo Wophimba Machimo,+ muzidzaliza lipengalo kuti limveke mʼdziko lanu lonse.