Levitiko 25:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Muzimuona ngati waganyu+ komanso ngati mlendo. Azikugwirirani ntchito mpaka Chaka cha Ufulu.