-
Levitiko 25:47Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
47 Koma ngati mlendo wokhala pakati panu walemera, ndipo mʼbale wanu amene akukhala naye pafupi wasauka nʼkudzigulitsa kwa mlendoyo, kapena kwa munthu wina wa mʼbanja la mlendoyo,
-