Levitiko 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ngati munthu amene akulonjezayo ndi wosauka moti sangakwanitse mtengo womwe unaikidwawo,+ azikaonetsa munthuyo kwa wansembe, ndipo wansembe azinena mtengo wake. Wansembe adzanena mtengo umene munthu amene analonjezayo angakwanitse.+
8 Koma ngati munthu amene akulonjezayo ndi wosauka moti sangakwanitse mtengo womwe unaikidwawo,+ azikaonetsa munthuyo kwa wansembe, ndipo wansembe azinena mtengo wake. Wansembe adzanena mtengo umene munthu amene analonjezayo angakwanitse.+