Levitiko 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ngati akufuna kuiwombola, azipereka mtengo wa nyamayo womwe unaikidwa nʼkuwonjezerapo limodzi mwa magawo 5 a mtengowo.+
13 Koma ngati akufuna kuiwombola, azipereka mtengo wa nyamayo womwe unaikidwa nʼkuwonjezerapo limodzi mwa magawo 5 a mtengowo.+