-
Levitiko 27:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Koma ngati munthu amene anapereka mundayo akufuna kuuwombola, azipereka mtengo wake womwe unaikidwa nʼkuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo ake 5, akatero mundawo uzikhala wake.
-