Numeri 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uwerenge+ gulu lonse la Aisiraeli* mogwirizana ndi mabanja awo, potengera nyumba za makolo awo, nʼkulemba mayina awo. Uwerenge amuna onse, mmodzi ndi mmodzi.
2 “Uwerenge+ gulu lonse la Aisiraeli* mogwirizana ndi mabanja awo, potengera nyumba za makolo awo, nʼkulemba mayina awo. Uwerenge amuna onse, mmodzi ndi mmodzi.