-
Numeri 1:45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Aisiraeli onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo mu Isiraeli, analembedwa mayina mogwirizana ndi nyumba za makolo awo.
-