Numeri 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Posamutsa chihema chokumanako,+ gulu la Alevi lizikhala pakati pa magulu enawo. Dongosolo limene azitsatira posamuka,+ ndi limenenso azitsatira pomanga misasa yawo, aliyense pamalo ake, mogwirizana ndi gulu lawo la mafuko atatu.
17 Posamutsa chihema chokumanako,+ gulu la Alevi lizikhala pakati pa magulu enawo. Dongosolo limene azitsatira posamuka,+ ndi limenenso azitsatira pomanga misasa yawo, aliyense pamalo ake, mogwirizana ndi gulu lawo la mafuko atatu.