-
Numeri 3:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Ana onse aamuna oyamba kubadwa amene anawawerenga, kuyambira a mwezi umodzi kupita mʼtsogolo, anakwana 22,273.