-
Numeri 3:50Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
50 Kwa ana aamuna oyamba kubadwa a Aisiraeli, analandira ndalama zokwana masekeli 1,365, mogwirizana ndi muyezo wa sekeli yakumalo oyera.
-