-
Numeri 3:51Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
51 Ndiyeno Mose anapereka ndalama za dipozo kwa Aroni ndi ana ake pomvera mawu a Yehova, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
-