-
Numeri 4:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 anawerenga onse kuyambira azaka 30 mpaka 50, amene anali mʼgulu la anthu amene anasankhidwa kuti azitumikira pachihema chokumanako.
-