Numeri 4:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Amenewa ndi anthu amene anawerengedwa kuchokera mʼmabanja a ana a Gerisoni, onse amene ankatumikira pachihema chokumanako. Mose ndi Aroni anawawerenga pomvera zimene Yehova analamula.+
41 Amenewa ndi anthu amene anawerengedwa kuchokera mʼmabanja a ana a Gerisoni, onse amene ankatumikira pachihema chokumanako. Mose ndi Aroni anawawerenga pomvera zimene Yehova analamula.+