Numeri 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Ngati mwamuna kapena mkazi wachita machimo alionse amene anthu amachita, nʼkuchita zinthu mosakhulupirika pamaso pa Yehova, munthu ameneyo wapalamula mlandu.+
6 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Ngati mwamuna kapena mkazi wachita machimo alionse amene anthu amachita, nʼkuchita zinthu mosakhulupirika pamaso pa Yehova, munthu ameneyo wapalamula mlandu.+