-
Numeri 5:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ngati mwamuna wake akuchita nsanje ndipo akukayikira kuti mkazi wake wachita chigololo nʼkudzidetsa pamene mkaziyo wachitadi chigololo, kapena ngati akuchita nsanje nʼkumakayikira kuti mkazi wake wachita chigololo pamene mkaziyo sanachite,
-