-
Numeri 5:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Kenako azitenga madzi opatulika mʼchiwiya chadothi. Azitengakonso fumbi lapansi mʼchihema, nʼkulithira mʼmadziwo.
-