Numeri 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Wansembeyo azilumbiritsa mkaziyo pomuuza kuti: “Ngati mwamuna aliyense sanagone nawe ndipo ngati sunamʼzembere mwamuna wako pamene uli mʼmanja mwake+ nʼkuchita chodetsa chilichonse, madzi owawa obweretsa tembererowa asakuvulaze.
19 Wansembeyo azilumbiritsa mkaziyo pomuuza kuti: “Ngati mwamuna aliyense sanagone nawe ndipo ngati sunamʼzembere mwamuna wako pamene uli mʼmanja mwake+ nʼkuchita chodetsa chilichonse, madzi owawa obweretsa tembererowa asakuvulaze.