Numeri 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Madzi a tembererowa alowe mʼmatumbo mwako kuti akatupitse mimba yako ndi kufotetsa* ntchafu* yako.” Ndipo mkaziyo aziyankha kuti: “Zikhale momwemo! Zikhale momwemo!”*
22 Madzi a tembererowa alowe mʼmatumbo mwako kuti akatupitse mimba yako ndi kufotetsa* ntchafu* yako.” Ndipo mkaziyo aziyankha kuti: “Zikhale momwemo! Zikhale momwemo!”*