Numeri 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno wansembeyo azitenga nsembe yambewu yansanje+ imene ili mʼmanja mwa mkaziyo, nʼkuiyendetsa uku ndi uku pamaso pa Yehova. Akatero, aziibweretsa pafupi ndi guwa lansembe.
25 Ndiyeno wansembeyo azitenga nsembe yambewu yansanje+ imene ili mʼmanja mwa mkaziyo, nʼkuiyendetsa uku ndi uku pamaso pa Yehova. Akatero, aziibweretsa pafupi ndi guwa lansembe.