Numeri 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Wansembeyo azitapako nsembe yambewuyo kuimira nsembe yonseyo, nʼkuiwotcha paguwa lansembe.+ Pambuyo pake, azipatsa mkaziyo madziwo kuti amwe.
26 Wansembeyo azitapako nsembe yambewuyo kuimira nsembe yonseyo, nʼkuiwotcha paguwa lansembe.+ Pambuyo pake, azipatsa mkaziyo madziwo kuti amwe.