Numeri 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lankhula ndi Aisiraeli ndipo uwauze kuti, ‘Ngati mwamuna kapena mkazi wachita lonjezo lapadera kwa Yehova lokhala Mnaziri,*+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2152
2 “Lankhula ndi Aisiraeli ndipo uwauze kuti, ‘Ngati mwamuna kapena mkazi wachita lonjezo lapadera kwa Yehova lokhala Mnaziri,*+