Numeri 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 asamamwe vinyo ndi zakumwa zina zoledzeretsa. Asamamwenso viniga* wokhala ndi vinyo, kapena viniga wochokera ku zakumwa zina zoledzeretsa,+ kapenanso madzi a mphesa. Ndiponso asamadye mphesa zaziwisi kapena zouma.
3 asamamwe vinyo ndi zakumwa zina zoledzeretsa. Asamamwenso viniga* wokhala ndi vinyo, kapena viniga wochokera ku zakumwa zina zoledzeretsa,+ kapenanso madzi a mphesa. Ndiponso asamadye mphesa zaziwisi kapena zouma.