Numeri 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ngati munthu wina wafera pambali pake+ mwadzidzidzi, moti Mnaziriyo wadetsa tsitsi limene lili ngati chizindikiro choti wadzipereka kwa Mulungu, azimeta tsitsi lakumutu kwake+ pa tsiku limene wayeretsedwa. Azilimeta pa tsiku la 7.
9 Koma ngati munthu wina wafera pambali pake+ mwadzidzidzi, moti Mnaziriyo wadetsa tsitsi limene lili ngati chizindikiro choti wadzipereka kwa Mulungu, azimeta tsitsi lakumutu kwake+ pa tsiku limene wayeretsedwa. Azilimeta pa tsiku la 7.