-
Numeri 6:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Kumeneko azipereka nsembe yake kwa Yehova. Azipereka nkhosa yaingʼono yamphongo yopanda chilema, yosapitirira chaka chimodzi, monga nsembe yopsereza.+ Aziperekanso mwana wa nkhosa wamkazi wopanda chilema, wosapitirira chaka chimodzi, monga nsembe yamachimo.+ Komanso azipereka nkhosa yamphongo yopanda chilema, monga nsembe yamgwirizano.+
-